Boma la Uganda lakana kuti apolisi anamumenya mkazi wa Bobi Wine |
Автор: Channel Africa
Загружено: 2026-01-29
Просмотров: 241
Описание:
Pomwe magulu omenyera ufulu amayi ku Uganda adzudzula boma kuti lisamachitire nkhaza amayi omwe akupanga nawo ndale, nduna yofalitsa uthenga ku Uganda a Chris Byaromunsi, yatsutsa kuti boma silinachitire nkhaza akazi awo a Bob Wine a Barbie Itungo.
Ndunayi yatsutsanso kuti a Kizza Besigye akudwala kachikena pomwe anangodwala chabe m'mimba masiku omwe malipoti amati a Besigye amadwala mwakayakaya. Mada Phiri walankhula ndi Alfred Dzaoneni mtolankhani wa Channel Africa ku m'mawa kwa Africa .
Повторяем попытку...
Доступные форматы для скачивания:
Скачать видео
-
Информация по загрузке: