WAKULA - CEN REE DON X FLEGOH
Автор: CEN REE DON
Загружено: 2026-02-05
Просмотров: 455
Описание:
Title :Wakula
Artist: Cen ree Don x flegoh
prod : on top records
video by uncle P
lyrics
intro (flegoh x Cen ree Don)
verse one(Cen ree Don)
hello a friend paja inu ndi aBoss//
simuphwekesa m'mapezeka ndima cross//
chomwe ndikufuna ndingofuna imozi//
ndizizimuse gulu by fire by force//
usaphwekesetu iwe Anthony//
ndingofuna zinthu zoti anthu andione//
masten ndiye akundikalipira//
akufuna mpongozi ati ine ndakula//
Pena kuzifusa koma ine ndi munthu//
kuumaku siza kumtundu//
kapena ndikufunika JuJu//
mayo mayo JuJu// X2
Pena kuzifusa koma ine ndi munthu//
kuumaku siza kumtundu//
kapena ndikufunika JuJu//
mayo mayo JuJu// X2
Hook (Cen ree Don)
Ndikangolakwa pang'ono Kwa masten ati Wakula ukwatire// ooh wooh wooh
Ndimafuna cross undivungireko Mwina nane ndigwire//
Nanga daily kumandikalipira kumandiraratira ati Wakula ukwatire//
ndiyeno a friend ndatopa nazo Pena ngati ndilire//
verse 2 ( flegoh)
nawe pena ukunyanya ,ukunyanya ukutichitisa manyazi//
ukuyenera ungomala basi ungomala nanga zoona kumasowa nkazi//
olo mbiri ya mimba ,kutipanga ngati ndife otchipa// amzakofe
man mumutriper ngati nkazi ndi uyo mumazimva // ahaaaah
chabwino sankha-sankha uyu ndi bulenda
koma kwawo nkwakachere //
utha kumapenga pachibwezi pokha koma
kubanja ndiye usakayese//
chabwino sankhani-sankha uyu ndi bulenda
koma kwawo nkwakachere //
utha kumapenga pachibwezi pokha koma
kubanja ndiye usakayese//
Hook (Cen ree Don)
Ndikangolakwa pang'ono Kwa masten ati Wakula ukwatire// ooh wooh wooh
Ndimafuna cross undivungireko Mwina nane ndigwire//
Nanga daily kumandikalipira kumandiraratira ati Wakula ukwatire//
ndiyeno a friend ndatopa nazo Pena ngati ndilire//ooh wooh wooh
Повторяем попытку...
Доступные форматы для скачивания:
Скачать видео
-
Информация по загрузке: