MISS MALAWI 2025 - THANDI CHISI WA WINA| MISS MALAWI GRAND FINALE AT BICC IN LILONGWE
Автор: AM TV MALAWI
Загружено: 2025-12-13
Просмотров: 20283
Описание:
#MissMalawi2025
Thandi Chisi ndiye chiphadzuwa cha dziko lino, Miss Malawi.
Thandi alandira mphotho yomwe akawonkhetsa zonse pamodzi ikukwana 50 million Kwacha.
Mwa ndalamayi, 30 million Kwacha, Thandi ndiyake pamene 10 million Kwacha ndiyoti agwilire ntchito ku Miss Malawi Foundation.
Ndalama ina, ayilipilira ofesi yake ku Area 43 kwa chaka chonse.
Thandi apezaso mwayi wa sukulu ku Zambia, ngati ali ndi Degree, akapanga Masters, ngati alibe degree, mwayi wake ndi omwewu.
Повторяем попытку...
Доступные форматы для скачивания:
Скачать видео
-
Информация по загрузке: