ycliper

Популярное

Музыка Кино и Анимация Автомобили Животные Спорт Путешествия Игры Юмор

Интересные видео

2025 Сериалы Трейлеры Новости Как сделать Видеоуроки Diy своими руками

Топ запросов

смотреть а4 schoolboy runaway турецкий сериал смотреть мультфильмы эдисон
Скачать

Khalabe Odikira - The Morning Star (Official Video)

Автор: The Morning Star - Mw

Загружено: 2023-10-20

Просмотров: 328358

Описание: Lyrics:
1. Zosautsa zochuluka okondedwa m'moyowu
Kukumana ndi zipsinjo zosaneneka
Kuyesetsa kupemphera ngati Mlungu saakumva
Zafika povuta moyuwu kuwawa

Kuyang’ana uko wachoka ndizogwetsa mphwayi
Kuganiza zatsogolo mtima umasweka
Nthawi zina ukaona ena zithu zikuwayendera
Zimangopangitsa ‘we kukhumudwa

Chorus
Kaya nyengo ivute iwopse bwanji
Ndi zinthu za kanthawi kanthawi kochepa
Zisakuchotse ‘we pamaso pa Mulengi wako
Khalabe odikira mkhulupire

Akulonjeza kukhala nawe kukusamalira zinthu zikavuta
Ngakhale lonjezano lake lichedwe bwanji
Khalabe odikira mkhulupire

2. Zolilitsa tsiku ndi tsiku kuopsedwa m'moyowu
Kunyozedwa ndiopembedza nao limodzi
Komabe m'nyengo zotere kumbuka liripo bwenzi
Bwenzi lopambana ndiye Yesu

Akhala nawe poyenda akhala nawe pogona
Akhala mawe mtendere ndinso polira
Iye ali ndi chinsisi cha tsogolo la moyo wako
Khalabe odikira mkhulupire
-----------------------------------------------------
The Morning Star, Kawale, Lilongwe
Audio by: Recall, Kuimba Mwamphamvu Studio
Video by: Hope Channel Malawi
-----------------------------------------------------
Share this video:
   • Khalabe Odikira - The Morning Star (Offici...  

Subscribe for more videos:
   / @themorningstar-mw  

Audio playlist:
   • M'bandakucha Album - The Morning Star  
-----------------------------------------------------
Connect with us:
Facebook:   / themorningstarsingersmw  
Instagram:   / themorningstar_mw  
Whatsapp: https://whatsapp.com/channel/0029Va5V...
Spotify - https://spotify.link/EC6GyW0v3xb

E-mail:
[email protected]

Не удается загрузить Youtube-плеер. Проверьте блокировку Youtube в вашей сети.
Повторяем попытку...
Khalabe Odikira - The Morning Star (Official Video)

Поделиться в:

Доступные форматы для скачивания:

Скачать видео

  • Информация по загрузке:

Скачать аудио

Похожие видео

LOYA WACHIMWENDO BANDA AKUKUZULA  JUDGE A MZONDI MVURA NDI POLICE PA NKHANI YA CHIMWENDO BANDA

LOYA WACHIMWENDO BANDA AKUKUZULA JUDGE A MZONDI MVURA NDI POLICE PA NKHANI YA CHIMWENDO BANDA

Msonkhano Wa Kale - The Morning Star (Official Video)

Msonkhano Wa Kale - The Morning Star (Official Video)

Hymn- Ndofamba Ndofamba

Hymn- Ndofamba Ndofamba

BON KALINDO 5 JANUARY 2026 KUSWAKUSWA MOIPA

BON KALINDO 5 JANUARY 2026 KUSWAKUSWA MOIPA

N'dzakondwa - Alex Mandala

N'dzakondwa - Alex Mandala

MPHAMVU YA KUMWAMBA - Pastor TY Nyirenda// CHIRIMBA Camp Meetings

MPHAMVU YA KUMWAMBA - Pastor TY Nyirenda// CHIRIMBA Camp Meetings

Ndidzam'dziwa  - The Morning Star (Official Video)

Ndidzam'dziwa - The Morning Star (Official Video)

BRIAN BANDA NDI ANZAKE ANG'ALURA IZI ZA JANE ANSAH PA HOT CURRENT LERO

BRIAN BANDA NDI ANZAKE ANG'ALURA IZI ZA JANE ANSAH PA HOT CURRENT LERO

DIKILANI (official video)

DIKILANI (official video)

CHIMWENDO ANACHEKERA MPAKA APA😂

CHIMWENDO ANACHEKERA MPAKA APA😂

Florence Massea - Mpulumutsi Wozizwitsa ndi Yesu (official lyric video)

Florence Massea - Mpulumutsi Wozizwitsa ndi Yesu (official lyric video)

Namasalima Singers  | Adzayankha

Namasalima Singers | Adzayankha

HOT CURRENT YA LERO PA 1 JANUARY ANG’ALURA MOSANYENGELERA MPAKA AULURASO ZODABWISA IZI

HOT CURRENT YA LERO PA 1 JANUARY ANG’ALURA MOSANYENGELERA MPAKA AULURASO ZODABWISA IZI

Mukuimiranji - The Morning Star (Official Video)

Mukuimiranji - The Morning Star (Official Video)

SHOW ME THERE - Beulah Land

SHOW ME THERE - Beulah Land

Machenjerero A Farawo  || Pastor TY Nyirenda Msonkhano Wamisasa Wapakanema -Tsiku Lachiwiri (Day 2)

Machenjerero A Farawo || Pastor TY Nyirenda Msonkhano Wamisasa Wapakanema -Tsiku Lachiwiri (Day 2)

Esther Chiyembekeza   Ndinkhondo kupemphera Video

Esther Chiyembekeza Ndinkhondo kupemphera Video

46 mins || Gospel old playlist SDA songs mix with various artists

46 mins || Gospel old playlist SDA songs mix with various artists

Yangosala mbiri yokha 2 - Philadelphia

Yangosala mbiri yokha 2 - Philadelphia

MADALITSO A YEHOVA - Pastor Ganamba

MADALITSO A YEHOVA - Pastor Ganamba

© 2025 ycliper. Все права защищены.

  • Контакты
  • О нас
  • Политика конфиденциальности

Контакты для правообладателей: [email protected]