BLACK STEEL - Sindu Fulumira(Vizualizer)
Автор: BLACK STEEL 🇲🇿
Загружено: 2025-07-18
Просмотров: 8432
Описание:
AJV ENTRETENIMENTO PRESENT:
Artista: BLACK STEEL
Titulo: SINDU FULUMIRA
Mix & Master: Jay S Yahelo Beat
Instrumental: EYOBLACK
Compositor: BLACK STEEL
Video production:
Video Maker: Black Wandrick
Letra:
Verse 1:
Ambuye… ndineyo mwana wanu…..
Ndango gwadha pano kuti… ndivepo mau anu;
Zonse zapadziko lino ndinuyo mwini wache.
Onse moyo wanga ine ndisiya M’manja mwanu yeah
Koma ine
Kuyenda ndekha ndalephera
Mpaka mphanvu zinandithera
Ndinu Chauta wazatheka
M’manja mwanu ndine otetezeka
Ine mwana wanu Yehova ndati
Kuyenda ndekha ndalephera
Mpaka mphanvu zinandithera
Koma baba
Corro:
Sundu fulumira aaah
(Sundu fulumira) koma ndikatani
(Koma ndikafika) oooh yehova baba
(Sindu fulumira aaah)
(Sundu fulumira) aaah
(Sundu fulumira) koma ndikatani
(Koma ndikafika) oooh yehova baba
(Sindu fulumira aaah)
Verse 2:
Adani wanga God sakucheza
Akufunitsitsa mutangondi leka
Kamoyoka katangrondi shokera, kundi shokera…
Mwina poti m’madalitso wanu ambiri
Awapanguitsa khala nsaje zawo zambiri
M’mesa kodi oyenda ndi inu aenda ndi didi ;
Mwina ndivuto khala mwana wanu dadi iih
Ndatopa nkugwah ine
(Mundigwire dzanja)
(Mundissasse babah)
(Ndekha simpambana)
Sindu Fulumira ine
Mundigwire dzanja)
(Mundissasse babah)
(Ndekha simpambana
Corro:
Sundu fulumira aaah
(Sundu fulumira) koma ndikatani
(Koma ndikafika) oooh yehova baba
(Sindu fulumira aaah)
(Sundu fulumira) aaah
(Sundu fulumira) koma ndikatani
(Koma ndikafika) oooh yehova baba
(Sindu fulumira aaah)
Ambuye….. ndi ineyo mwana wanu ;
Ndivepo mau anu;
Ndi inuyo mwini wache
#music #malawi #zambia #nigeria
@DriemoMw @praiseumali @GwambaOfficial @kellkay5565 @namadingo @kaygletras @GitessBambo @ajventretenimento @kamanekamas @yomapsyo3164 @dplatnumz
Повторяем попытку...
Доступные форматы для скачивания:
Скачать видео
-
Информация по загрузке: