Ndikhulupilira Bible (Official Video) — Area 47 Senior Youth Choir
Автор: Area 47 Senior Youth Choir
Загружено: 2026-02-20
Просмотров: 9728
Описание:
Words & Music: Ndudirim Nwachukwu
Accessed from: Tunefulness.scores
Title: Oh yes, I believe
@tunefulness.scores
_________________________________________
Chichewa Lyrics:
1. Ndikhulupilira Bible,
Ndukhulupilira Yesu,
Kuti anafa pamtanda kufera 'ne.
Ndikhulupirira Tate, Mwana ndi Mzimu Oyera,
Ine, ine, ndikhulupira.
Chorus
Kuti anandiferane,
Kuti ndikhale ndi moyo.
Anafa, anafa, anafa kufera ine,
Akufuna ndisiye tchimo, anafa pamtanda paja,
Nagwazidwa Mbuye wanga.
2. Ndikhulipilira Yesu,
Abweradi posachedwa,
Kudzatenga onse kunka nawo mwamba.
Kuti tikhale ndi moyo,
Osatha mudziko ilo,
Ine ine ndikhulupira.
Повторяем попытку...
Доступные форматы для скачивания:
Скачать видео
-
Информация по загрузке: