Umboni wa Mayi Mawindo - za Gahena ndi Paradaizo
Автор: Living for Christ - Malawi
Загружено: 2023-06-19
Просмотров: 17976
Описание:
Nawu umboni wa Mayi Mawindo womwe adaupereka pa wailesi ya FM 101. Mu umboniwu, akufotokoza za Gahena komanso Paradaizo.
Ku Mateyu 13:42, Ambuye Yesu akufotokoza za ng'anjo ya moto momwe anthu onse ochimwa adzaponyedwe "kumene kudzakhala kulira ndi kukukuta mano." Verse ya 43 ikupitilira motere: "Pomwepo olungamawo adzawalitsa monga dzuwa, mu Ufumu wa Atate wao. Amene ali ndi makutu amve."
Повторяем попытку...
Доступные форматы для скачивания:
Скачать видео
-
Информация по загрузке: