ycliper

Популярное

Музыка Кино и Анимация Автомобили Животные Спорт Путешествия Игры Юмор

Интересные видео

2025 Сериалы Трейлеры Новости Как сделать Видеоуроки Diy своими руками

Топ запросов

смотреть а4 schoolboy runaway турецкий сериал смотреть мультфильмы эдисон
Скачать

Nkhani Ya Kulezebwa Kwa nyooh Kwa Mlaka Maliro

Автор: Hanifa Mw

Загружено: 2022-10-23

Просмотров: 43812

Описание: MLAKA AKANIKA KUYIMBA KAMBA KOLEDZERA
Pamene woyimba wa pakanthawi Mlaka Maliro akuyetsanso kuti anthu amukonde mmayimbidwe ake potsatira kusiya kukhala m’busa wa mpingo wa Enligtened Christian Gathering (ECG) mkuyambanso kumayenda ma show, kumapeto kwa masabata apitawa wakhumudwitsa anthu atakanika kuyimba ku Octagon Tower m’boma la Mangochi zomwe zikuwonesa kuti anali ataledzera kwambiri . Kumayambiliro kwa sabata ino mmasamba amchezo a Facebook komanso Whatsapp kwakhala kukuyenda ma kanema angapo omwe akuonetsa woyimbayu akuchita kukanika kuyimba nyimbo zake zomwe pa stage ndipo anthu ena anayamba kumukuwa kuti asiye popeza wamwa kabanga.

Не удается загрузить Youtube-плеер. Проверьте блокировку Youtube в вашей сети.
Повторяем попытку...
Nkhani Ya Kulezebwa Kwa nyooh Kwa Mlaka Maliro

Поделиться в:

Доступные форматы для скачивания:

Скачать видео

  • Информация по загрузке:

Скачать аудио

Похожие видео

KUKAMBA ZA M'BANJA  NDI MIYAMBO YA A ANTHU A MTUNDU WA CHILHOMWE

KUKAMBA ZA M'BANJA NDI MIYAMBO YA A ANTHU A MTUNDU WA CHILHOMWE

CRUISE 5 WITH MLAKA MALIRO PART  1

CRUISE 5 WITH MLAKA MALIRO PART 1

Times Exclusive with Mlaka Maliro - 9 April 2022

Times Exclusive with Mlaka Maliro - 9 April 2022

Mlaka Maliro - Si Uyu ( Official Music Video ) Dir VJ Ken

Mlaka Maliro - Si Uyu ( Official Music Video ) Dir VJ Ken

YAHWEH,BENADETTA MLAKA MALIRO

YAHWEH,BENADETTA MLAKA MALIRO

Amayi Tokotani

Amayi Tokotani

Chiphwilikiti mu Nzinda wa Limbe

Chiphwilikiti mu Nzinda wa Limbe

MLAKA MALIRO_THERE'S NO WINE_(OFFICIAL VISUAL)_ DIR VJ KEN

MLAKA MALIRO_THERE'S NO WINE_(OFFICIAL VISUAL)_ DIR VJ KEN

CRUISE 5 WITH DR. BEN PHIRI

CRUISE 5 WITH DR. BEN PHIRI

Uladi Mussa at MCP, Kumachenjera pa town

Uladi Mussa at MCP, Kumachenjera pa town

Mlaka Maliro live

Mlaka Maliro live

Cruise 5 with Ruth Walker Jiyani

Cruise 5 with Ruth Walker Jiyani

MLAKA MALIRO LIVE ON STAGE

MLAKA MALIRO LIVE ON STAGE

СОЮЗНИКИ КИНУЛИ США: ПОЧЕМУ НАТО НЕ ПОДДЕРЖАЛИ США ПРОТИВ ИРАНА - Аналитический обзор

СОЮЗНИКИ КИНУЛИ США: ПОЧЕМУ НАТО НЕ ПОДДЕРЖАЛИ США ПРОТИВ ИРАНА - Аналитический обзор

The Court (Zam'banja)

The Court (Zam'banja)

BISHOP ZAKARIYA MTUKULA vs SH.MUSTAFA DAILESI

BISHOP ZAKARIYA MTUKULA vs SH.MUSTAFA DAILESI

KULIBE SONG from my album Yahweh

KULIBE SONG from my album Yahweh

ХУДШЕЕ  СЛУЧИЛОСЬ⚡️СОСКИН: ТРАМП - «ЗЕЛЕНСКИЙ ДОЛЖЕН УЙТИ СЕЙЧАС»! ДЕПУТАТЫ ИДУТ НА ФРОНТ!

ХУДШЕЕ СЛУЧИЛОСЬ⚡️СОСКИН: ТРАМП - «ЗЕЛЕНСКИЙ ДОЛЖЕН УЙТИ СЕЙЧАС»! ДЕПУТАТЫ ИДУТ НА ФРОНТ!

Kalata ya oBwande 16 March 2026

Kalata ya oBwande 16 March 2026

Гениальная самоделка Ирана: Самое ненавистное оружие 21 века, которое переписало правила войны

Гениальная самоделка Ирана: Самое ненавистное оружие 21 века, которое переписало правила войны

© 2025 ycliper. Все права защищены.

  • Контакты
  • О нас
  • Политика конфиденциальности

Контакты для правообладателей: [email protected]