John Chilembwe Documentary
Автор: MalawiNation
Загружено: 2026-01-15
Просмотров: 3756
Описание:
Patha zaka 110 kuchokera pomwe m’busa John Chilembwe adaphedwa m’chaka cha 1915 akumenya nkhondo yolimbana ndi atsamunda.
Pomwe pa 15 January chaka ndi chaka aMalawi amakumbukira Chilembwe, papezeka mbali ziwiri zomwe zikunena kuti ndiwo mbumba yeniyeni ya Chilembwe.
Gulu lina ndi la m’midzi ya Mpelule ndi Chikapa kwa T/A Chikowi ku Zomba.
Pomwe lina ndi la m’mudzi mwa Mkwaila, T/A Kadewere ku Chiradzulu.
Wonerani kanemuyu kuti mumve zambiri.
Повторяем попытку...
Доступные форматы для скачивания:
Скачать видео
-
Информация по загрузке: